-
Luka 8:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 “Pita kunyumba ndipo ukafotokoze zimene Mulungu wakuchitira.” Choncho munthu uja anapitadi ndipo ankafalitsa mumzinda wonsewo zimene Yesu anamuchitira.
-