Luka 8:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiyeno panali mayi wina amene ankadwala matenda otaya magazi+ kwa zaka 12, ndipo palibe aliyense amene anatha kumuchiritsa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:43 Yesu—Ndi Njira, tsa. 116 Nsanja ya Olonda,6/1/1987, tsa. 24
43 Ndiyeno panali mayi wina amene ankadwala matenda otaya magazi+ kwa zaka 12, ndipo palibe aliyense amene anatha kumuchiritsa.+