Luka 8:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Koma anthu onse ankalira komanso kudziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni. Choncho Yesu anawauza kuti: “Tontholani,+ chifukwa mwanayu sanamwalire, koma akugona.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:52 Yesu—Ndi Njira, tsa. 118 Nsanja ya Olonda,6/15/1987, tsa. 22
52 Koma anthu onse ankalira komanso kudziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni. Choncho Yesu anawauza kuti: “Tontholani,+ chifukwa mwanayu sanamwalire, koma akugona.”+