Luka 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukafika panyumba iliyonse, muzikhala mʼnyumbayo mpaka nthawi yochoka kumeneko itakwana.+