Luka 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chifukwa aliyense wochita manyazi ndi ine komanso mawu anga, Mwana wa munthu adzachita nayenso manyazi akadzabwera mu ulemerero wake, wa Atate wake ndi wa angelo oyera.+
26 Chifukwa aliyense wochita manyazi ndi ine komanso mawu anga, Mwana wa munthu adzachita nayenso manyazi akadzabwera mu ulemerero wake, wa Atate wake ndi wa angelo oyera.+