-
Luka 9:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Koma ophunzirawo sanamvetse zimene anawauzazo. Tanthauzo lake linali lobisika kwa iwo kuti asazindikire ndipo ankaopa kumufunsa za mawu amenewa.
-