Luka 9:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Koma Yesu anamuuza kuti: “Nkhandwe zili ndi mapanga ndipo mbalame zamumlengalenga zili ndi zisa, koma Mwana wa munthu alibiretu poti nʼkutsamiritsa mutu wake.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:58 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 154-155 Nsanja ya Olonda,3/15/1988, tsa. 24
58 Koma Yesu anamuuza kuti: “Nkhandwe zili ndi mapanga ndipo mbalame zamumlengalenga zili ndi zisa, koma Mwana wa munthu alibiretu poti nʼkutsamiritsa mutu wake.”+