Luka 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anawauza kuti: “Inde, pali zinthu zambiri zofunika kukolola, koma antchito ndi ochepa. Choncho pemphani Mwiniwake wa munda kuti atumize antchito kukakolola.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:2 Nsanja ya Olonda,3/1/1998, tsa. 30
2 Kenako anawauza kuti: “Inde, pali zinthu zambiri zofunika kukolola, koma antchito ndi ochepa. Choncho pemphani Mwiniwake wa munda kuti atumize antchito kukakolola.+