Luka 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chifukwa ndithu ndikukuuzani, aneneri ambiri komanso mafumu ankalakalaka kuti aone zinthu zimene mukuziona inuzi koma sanazione,+ komanso kuti amve zimene mukumva inuzi koma sanazimve.” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:24 Nsanja ya Olonda,2/1/2007, ptsa. 22-23
24 Chifukwa ndithu ndikukuuzani, aneneri ambiri komanso mafumu ankalakalaka kuti aone zinthu zimene mukuziona inuzi koma sanazione,+ komanso kuti amve zimene mukumva inuzi koma sanazimve.”