Luka 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako munthu wina wodziwa Chilamulo anaimirira kuti amuyese ndipo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, ndizichita chiyani kuti ndidzapeze moyo wosatha?”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:25 Yesu—Ndi Njira, tsa. 172 Nsanja ya Olonda,7/15/1988, tsa. 243/1/1986, tsa. 27
25 Kenako munthu wina wodziwa Chilamulo anaimirira kuti amuyese ndipo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, ndizichita chiyani kuti ndidzapeze moyo wosatha?”+