-
Luka 10:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ndiye zinangochitika kuti wansembe wina ankadutsa mumsewu womwewo, koma atamuona, anangomulambalala.