-
Luka 12:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 ndiye ndidzadziuza kuti: “Uli ndi zinthu zambiri zabwino ndipo zisungika kwa zaka zambiri. Mtima mʼmalo, udye, umwe ndi kusangalala.”’
-