-
Luka 12:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Osangalala ndi akapolo amene mbuye wawo pobwera adzawapeza akudikira! Ndithu ndikukuuzani, iye adzavala epuloni kuti agwire ntchito ndipo adzawakhazika patebulo kuti adye chakudya nʼkumawatumikira.
-