-
Luka 12:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Kenako anauzanso gulu la anthulo kuti: “Mukaona mtambo ukukwera chakumadzulo, nthawi yomweyo mumanena kuti, ‘Kukubwera chimvula,’ ndipo chimabweradi.
-