-
Luka 13:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Pa nthawiyo, ena mwa anthu amene anali pamenepo anamufotokozera za Agalileya amene magazi awo, Pilato anawasakaniza ndi nsembe zawo.
-