-
Luka 13:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Iye anawayankha kuti: “Pitani mukaiuze nkhandwe imeneyo kuti, ‘Ine ndikutulutsa ziwanda ndi kuchiritsa anthu lero ndi mawa, ndipo ndimaliza tsiku lachitatu.’
-