-
Luka 14:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiyeno kapolo uja anabwerera kukanena zimenezi kwa mbuye wake. Mwininyumbayo atamva zimenezi anakwiya ndipo anauza kapolo wakeyo kuti, ‘Pita mwamsanga mʼmisewu ndi mʼnjira zamumzindawu, ukatenge anthu osauka, otsimphina, osaona komanso olumala nʼkubwera nawo kuno.’
-