-
Luka 17:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Nʼzosatheka kuti pakhale popanda zopunthwitsa. Koma tsoka kwa munthu amene zopunthwitsazo zimadzera mwa iye!
-