Luka 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Samalani ndithu. Ngati mʼbale wako wachita tchimo umudzudzule+ ndipo akalapa umukhululukire.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:3 Galamukani!,8/8/1995, tsa. 10