-
Luka 17:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kodi sadzamuuza kuti, ‘Ndikonzere chakudya chamadzulo, uvale epuloni nʼkunditumikira mpaka nditamaliza kudya ndi kumwa, pambuyo pake iwenso udye ndi kumwaʼ?
-