Luka 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamene ankalowa mʼmudzi winawake, anakumana ndi amuna 10 akhate koma iwo anaima chapatali ndithu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:12 Yesu—Ndi Njira, tsa. 216 Nsanja ya Olonda,6/1/1989, tsa. 8
12 Pamene ankalowa mʼmudzi winawake, anakumana ndi amuna 10 akhate koma iwo anaima chapatali ndithu.+