Luka 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Afarisi atamufunsa kuti Ufumu wa Mulungu udzabwera liti,+ iye anawayankha kuti: “Ufumu wa Mulungu sudzabwera mwa maonekedwe ochititsa chidwi. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:20 Yesu—Ndi Njira, tsa. 218 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, tsa. 8
20 Afarisi atamufunsa kuti Ufumu wa Mulungu udzabwera liti,+ iye anawayankha kuti: “Ufumu wa Mulungu sudzabwera mwa maonekedwe ochititsa chidwi.