Luka 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mʼmasiku amenewo anthu ankadya ndi kumwa. Amuna ankakwatira ndipo akazi ankakwatiwa mpaka tsiku limene Nowa analowa mʼchingalawa,+ ndipo Chigumula chinabwera nʼkuwononga anthu onsewo.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:27 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 218-219 Nsanja ya Olonda,6/15/1989, ptsa. 8-9
27 Mʼmasiku amenewo anthu ankadya ndi kumwa. Amuna ankakwatira ndipo akazi ankakwatiwa mpaka tsiku limene Nowa analowa mʼchingalawa,+ ndipo Chigumula chinabwera nʼkuwononga anthu onsewo.+