-
Luka 19:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Yesu atafika pamalopo, anayangʼana mʼmwambamo nʼkumuuza kuti: “Zakeyu, fulumira tsika, chifukwa lero ndikuyenera kukakhala mʼnyumba mwako.”
-