-
Luka 19:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma anthu amʼdziko lakwawo anadana naye ndipo iye atapita anatumiza akazembe kuti akanene kuti, ‘Ife sitikufuna kuti munthu ameneyu akhale mfumu yathu.’
-