Luka 19:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atabwerera kwawo pambuyo polandira ufumuwo, anaitana akapolo amene anawapatsa ndalama* aja kuti abwere kwa iye, kuti awerengerane nʼkuona mmene apindulira pa malonda awo.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:15 Nsanja ya Olonda,3/15/1990, tsa. 15
15 Atabwerera kwawo pambuyo polandira ufumuwo, anaitana akapolo amene anawapatsa ndalama* aja kuti abwere kwa iye, kuti awerengerane nʼkuona mmene apindulira pa malonda awo.+