Luka 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Woyamba anabwera ndipo ananena kuti, ‘Mbuyanga, ndalama yanu ya mina ija yapindula ndalama zina zokwana ma mina 10.’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:16 Yesu—Ndi Njira, tsa. 232 Nsanja ya Olonda,10/1/1989, tsa. 8
16 Woyamba anabwera ndipo ananena kuti, ‘Mbuyanga, ndalama yanu ya mina ija yapindula ndalama zina zokwana ma mina 10.’+