Luka 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anamuuza kuti, ‘Wachita bwino, ndiwe kapolo wabwino! Chifukwa wasonyeza kuti ndiwe wokhulupirika pa chinthu chachingʼono, ndikupatsa ulamuliro woyangʼanira mizinda 10.’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:17 Yesu—Ndi Njira, tsa. 232 Nsanja ya Olonda,10/1/1989, tsa. 8
17 Iye anamuuza kuti, ‘Wachita bwino, ndiwe kapolo wabwino! Chifukwa wasonyeza kuti ndiwe wokhulupirika pa chinthu chachingʼono, ndikupatsa ulamuliro woyangʼanira mizinda 10.’+