Luka 19:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiye nʼchifukwa chiyani sunasungitse ndalama yangayo* kubanki? Ukanatero, ine pobwera ndikanaitenga limodzi ndi chiwongoladzanja chake.’ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:23 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 232-233 Nsanja ya Olonda,10/1/1989, ptsa. 8-9
23 Ndiye nʼchifukwa chiyani sunasungitse ndalama yangayo* kubanki? Ukanatero, ine pobwera ndikanaitenga limodzi ndi chiwongoladzanja chake.’