Luka 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atatero anauza anthu amene anaima chapafupi kuti, ‘Mulandeni ndalama ya minayo nʼkuipereka kwa amene ali ndi ndalama za mina 10.’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:24 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 232-233 Nsanja ya Olonda,10/1/1989, ptsa. 8-9
24 Atatero anauza anthu amene anaima chapafupi kuti, ‘Mulandeni ndalama ya minayo nʼkuipereka kwa amene ali ndi ndalama za mina 10.’+