Luka 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno atayandikira ku Betefage ndi Betaniya paphiri lotchedwa phiri la Maolivi,+ anatumiza ophunzira ake awiri.+
29 Ndiyeno atayandikira ku Betefage ndi Betaniya paphiri lotchedwa phiri la Maolivi,+ anatumiza ophunzira ake awiri.+