-
Luka 19:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Iye anawauza kuti: “Pitani mʼmudzi umene mukuuonawo, ndipo mukalowa mmenemo mukapeza bulu wamngʼono wamphongo atamumangirira, amene munthu sanakwerepo chiyambire. Mukamumasule nʼkubwera naye kuno.
-