-
Luka 20:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ iye atifunsa kuti, ‘Nanga nʼchifukwa chiyani simunamukhulupirire?’
-