Luka 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno iye anayamba kuuza anthuwo fanizo ili: “Munthu wina analima munda wa mpesa+ ndipo anausiya mʼmanja mwa alimi nʼkupita kudziko lina kumene anakhalako nthawi yaitali ndithu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:9 Yesu—Ndi Njira, tsa. 246 Nsanja ya Olonda,1/1/1990, tsa. 8
9 Ndiyeno iye anayamba kuuza anthuwo fanizo ili: “Munthu wina analima munda wa mpesa+ ndipo anausiya mʼmanja mwa alimi nʼkupita kudziko lina kumene anakhalako nthawi yaitali ndithu.+