Luka 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiye nyengo ya zipatso itakwana, anatumiza kapolo wake kwa alimiwo kuti akamupatseko zina mwa zipatso zamʼmunda wa mpesawo. Koma alimiwo anamumenya nʼkumubweza chimanjamanja.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:10 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 246-247 Nsanja ya Olonda,1/1/1990, ptsa. 8-9
10 Ndiye nyengo ya zipatso itakwana, anatumiza kapolo wake kwa alimiwo kuti akamupatseko zina mwa zipatso zamʼmunda wa mpesawo. Koma alimiwo anamumenya nʼkumubweza chimanjamanja.+