Luka 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iye anawatumiziranso kapolo wina. Ameneyonso anamumenya nʼkumuchitira zachipongwe,* ndipo anamubweza chimanjamanja.
11 Koma iye anawatumiziranso kapolo wina. Ameneyonso anamumenya nʼkumuchitira zachipongwe,* ndipo anamubweza chimanjamanja.