Luka 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zitatero mwiniwake wa munda wa mpesa uja anati, ‘Ndichite chiyani tsopano? Chabwino, nditumiza mwana wanga wokondedwa.+ Mosakayikira mwana wanga yekhayu akamulemekeza.’
13 Zitatero mwiniwake wa munda wa mpesa uja anati, ‘Ndichite chiyani tsopano? Chabwino, nditumiza mwana wanga wokondedwa.+ Mosakayikira mwana wanga yekhayu akamulemekeza.’