-
Luka 20:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Alimiwo atamuona anayamba kukambirana kuti, ‘Eyaa, uyu ndi amene adzalandire cholowa. Tiyeni timuphe kuti cholowacho chikhale chathu.’
-