Luka 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma iye anawayangʼanitsitsa nʼkunena kuti: “Paja malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana, wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.’*+ Kodi mawu amenewa amatanthauza chiyani? Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2017, ptsa. 9-10
17 Koma iye anawayangʼanitsitsa nʼkunena kuti: “Paja malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana, wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.’*+ Kodi mawu amenewa amatanthauza chiyani?