Luka 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anawayankha kuti: “Ana a mʼnthawi* ino amakwatira ndi kukwatiwa.