Luka 20:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma zakuti akufa amaukitsidwa ngakhalenso Mose anafotokoza munkhani ya chitsamba cha minga, pamene ananena kuti Yehova* ndi ‘Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo.’+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:37 Nsanja ya Olonda,5/1/2005, tsa. 133/1/1986, ptsa. 28-29
37 Koma zakuti akufa amaukitsidwa ngakhalenso Mose anafotokoza munkhani ya chitsamba cha minga, pamene ananena kuti Yehova* ndi ‘Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo.’+