Luka 23:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Ndiyeno panali mwamuna wina dzina lake Yosefe, amene anali wa mʼKhoti Lalikulu la Ayuda. Munthu ameneyu anali wabwino komanso wolungama.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:50 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, tsa. 18
50 Ndiyeno panali mwamuna wina dzina lake Yosefe, amene anali wa mʼKhoti Lalikulu la Ayuda. Munthu ameneyu anali wabwino komanso wolungama.+