Luka 23:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Choncho anautsitsa+ nʼkuukulunga munsalu yabwino kwambiri ndipo anakauika mʼmanda*+ amene anawagoba muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chiyambire. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:53 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),10/2017, ptsa. 19-20
53 Choncho anautsitsa+ nʼkuukulunga munsalu yabwino kwambiri ndipo anakauika mʼmanda*+ amene anawagoba muthanthwe, mmene anali asanaikemo munthu chiyambire.