Luka 23:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Tsopano linali Tsiku Lokonzekera,+ ndipo Sabata+ linali litatsala pangʼono kuyamba.