Yohane 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho Ayuda anayamba kuuza munthu amene anachiritsidwa uja kuti: “Lero ndi Sabata, nʼzosaloleka kuti unyamule machirawa.”+
10 Choncho Ayuda anayamba kuuza munthu amene anachiritsidwa uja kuti: “Lero ndi Sabata, nʼzosaloleka kuti unyamule machirawa.”+