Yohane 11:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako Yesu atadzumanso povutika mumtima, anafika kumandako.* Kwenikweni linali phanga, ndipo analitseka ndi chimwala. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:38 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 30
38 Kenako Yesu atadzumanso povutika mumtima, anafika kumandako.* Kwenikweni linali phanga, ndipo analitseka ndi chimwala.