Yohane 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Afarisi anayamba kukambirana kuti: “Apatu ndiye mukudzionera nokha kuti palibe chimene tikuphulapo. Onani! Dziko lonse likumutsatira.”+
19 Choncho Afarisi anayamba kukambirana kuti: “Apatu ndiye mukudzionera nokha kuti palibe chimene tikuphulapo. Onani! Dziko lonse likumutsatira.”+