Yohane 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ine ndikhale wogwirizana ndi iwo, inu mukhale wogwirizana ndi ine, kuti iwo akhale mumgwirizano weniweni,* kuti dziko lidziwe kuti inu munandituma ine komanso kuti mumawakonda ngati mmene mumandikondera ine. Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:23 Nsanja ya Olonda,10/15/2013, ptsa. 29-30
23 Ine ndikhale wogwirizana ndi iwo, inu mukhale wogwirizana ndi ine, kuti iwo akhale mumgwirizano weniweni,* kuti dziko lidziwe kuti inu munandituma ine komanso kuti mumawakonda ngati mmene mumandikondera ine.