Yohane 19:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Nikodemo+ amene anabwera kwa iye usiku poyamba paja, anabweranso atatenga mule wosakaniza ndi aloye, wopitirira makilogalamu 32.*+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:39 Yesu—Ndi Njira, tsa. 303 Nsanja ya Olonda,2/1/2002, ptsa. 10-11
39 Nikodemo+ amene anabwera kwa iye usiku poyamba paja, anabweranso atatenga mule wosakaniza ndi aloye, wopitirira makilogalamu 32.*+