Machitidwe 2:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choncho amene analandira mawu akewo mosangalala anabatizidwa,+ moti tsiku limenelo chiwerengero cha ophunzirawo chinawonjezereka ndi anthu pafupifupi 3,000.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:41 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 26-27 Nsanja ya Olonda,8/1/2002, ptsa. 15-16
41 Choncho amene analandira mawu akewo mosangalala anabatizidwa,+ moti tsiku limenelo chiwerengero cha ophunzirawo chinawonjezereka ndi anthu pafupifupi 3,000.+